Mateyu 26:44 - Buku Lopatulika44 Ndipo anawasiyanso, napemphera kachitatu, nateronso mau omwewo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201444 Ndipo anawasiyanso, napemphera kachitatu, nateronso mau omwewo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa44 Yesu adaŵasiyanso, napita kukapemphera kachitatu, akunena mau amodzimodzi omwe aja. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero44 Choncho anawasiya napitanso kukapemphera kachitatu nanenanso chimodzimodzi. Onani mutuwo |