Mateyu 26:41 - Buku Lopatulika41 Chezerani ndi kupemphera, kuti mungalowe m'kuyesedwa: mzimutu uli wakufuna, koma thupi lili lolefuka. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201441 Chezerani ndi kupemphera, kuti mungalowe m'kuyesedwa: mzimutu uli wakufuna, koma thupi lili lolefuka. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa41 Khalani maso inu ndi kumapemphera, kuti mungagwe m'zokuyesani. Mtima ndiye ukufunitsitsadi, koma langokhala lofooka ndi thupi.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero41 Khalani maso ndi kupemphera kuti musagwe mʼmayesero. Mzimu ukufuna koma thupi ndi lofowoka.” Onani mutuwo |