Mateyu 26:34 - Buku Lopatulika34 Yesu anati kwa iye, Indetu ndinena kwa iwe, kuti usiku uno, tambala asanalire, udzandikana Ine katatu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201434 Yesu anati kwa iye, Indetu ndinena kwa iwe, kuti usiku uno, tambala asanalire, udzandikana Ine katatu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa34 Yesu adamuuza kuti, “Ndithu ndikunenetsa kuti usiku womwe uno, tambala asanalire, ukhala utandikana katatu kuti Ine sundidziŵa.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero34 Yesu anayankha nati, “Zoonadi, ndikukuwuza kuti usiku omwe uno, asanalire tambala, udzandikana Ine katatu.” Onani mutuwo |