Mateyu 26:35 - Buku Lopatulika35 Petro ananena kwa Iye, Ngakhale ine ndikafa ndi Inu, sindidzakukanani Inu iai. Anateronso ophunzira onse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201435 Petro ananena kwa Iye, Ngakhale ine ndikafa ndi Inu, sindidzakukanani Inu iai. Anateronso ophunzira onse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa35 Koma Petro adamuuza kuti, “Ngakhale atati andiphere nanu kumodzi, ine sindingakukaneni konse kuti sindikudziŵani.” Ophunzira ena onse aja nawonso adanena chimodzimodzi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero35 Koma Petro ananenetsa nati, “Ngakhale kutakhala kufa nanu pamodzi, sindidzakukanani.” Ndipo ophunzira onse ananena chimodzimodzi. Onani mutuwo |