Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Mateyu 26:23 - Buku Lopatulika

23 Ndipo Iye anayankha nati, Iye amene asunsa pamodzi ndi Ine dzanja lake m'mbale, yemweyu adzandipereka Ine.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

23 Ndipo Iye anayankha nati, Iye amene asunsa pamodzi ndi Ine dzanja lake m'mbale, yemweyu adzandipereka Ine.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

23 Yesu adaŵayankha kuti, “Yemwe wasunsa mkate m'mbalemu pamodzi ndi Ine, ameneyo ndiye andipereke.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

23 Yesu anayankha nati, “Iye amene akusunsa mʼmbale pamodzi ndi Ine, yemweyo adzandipereka.

Onani mutuwo Koperani




Mateyu 26:23
6 Mawu Ofanana  

Ngakhale bwenzi langa lenileni, amene ndamkhulupirira, ndiye amene adadyako mkate wanga, anandikwezera chidendene chake.


Waulesi alonga dzanja lake m'mbale, osalibwezanso kukamwa kwake.


Ndipo iwo anagwidwa ndi chisoni chachikulu, nayamba kunena kwa Iye mmodzimmodzi, Kodi ndine, Ambuye?


Koma onani, dzanja lake la iye amene adzandipereka ali pagome pano pamodzi ndi Ine.


Sindinena za inu nonse; ndidziwa amene ndawasankha: koma kuti cholemba chikwaniridwe, Iye wakudya mkate wanga anatsalimira pa Ine chidendene chake.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa