Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Mateyu 26:22 - Buku Lopatulika

22 Ndipo iwo anagwidwa ndi chisoni chachikulu, nayamba kunena kwa Iye mmodzimmodzi, Kodi ndine, Ambuye?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

22 Ndipo iwo anagwidwa ndi chisoni chachikulu, nayamba kunena kwa Iye mmodzimmodzi, Kodi ndine, Ambuye?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

22 Ophunzirawo adamva chisoni kwambiri, nayamba mmodzimmodzi kumufunsa kuti, “Monga nkukhala ine, Ambuye?”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

22 Iwo anamva chisoni kwambiri ndipo anayamba kuyankhulana naye mmodzimmodzi nati, “Kodi nʼkukhala ine Ambuye?”

Onani mutuwo Koperani




Mateyu 26:22
7 Mawu Ofanana  

ndipo m'mene analinkudya, Iye anati, Indetu ndinena kwa inu, mmodzi wa inu adzandipereka Ine.


Ndipo Iye anayankha nati, Iye amene asunsa pamodzi ndi Ine dzanja lake m'mbale, yemweyu adzandipereka Ine.


Ndipo anayamba kufunsana mwa iwo okha, ndiye yani mwa iwo amene adzachita ichi.


Ananena naye kachitatu, Simoni mwana wa Yona, kodi undikonda Ine? Petro anamva chisoni kuti anati kwa iye kachitatu, Kodi undikonda Ine? Ndipo anati kwa iye, Ambuye, mudziwa Inu zonse; muzindikira kuti ndikukondani Inu. Yesu ananena naye, Dyetsa nkhosa zanga.


Koma munthu adziyese yekha, ndi kotero adye mkate, ndi kumwera chikho.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa