Mateyu 26:20 - Buku Lopatulika20 Ndipo pakufika madzulo, Iye analinkukhala pachakudya pamodzi ndi ophunzira khumi ndi awiri; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 Ndipo pakufika madzulo, Iye analinkukhala pachakudya pamodzi ndi ophunzira khumi ndi awiri; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 Kutada, Yesu ndi ophunzira ake khumi ndi aŵiri aja adakhala pamodzi nkumadya. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 Kutada, Yesu ndi ophunzira ake khumi ndi awiriwo anakhala pa tebulo nʼkumadya. Onani mutuwo |