Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Mateyu 26:19 - Buku Lopatulika

19 Ndipo ophunzira anachita monga Yesu anawauza, nakonza Paska.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

19 Ndipo ophunzira anachita monga Yesu anawauza, nakonza Paska.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

19 Ophunzira aja adapita nakachita zomwe Yesu adaaŵauza, nakakonzadi za phwando la Paska.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

19 Pamenepo ophunzira ake anachita monga momwe Yesu anawawuzira ndipo anakonza Paska.

Onani mutuwo Koperani




Mateyu 26:19
7 Mawu Ofanana  

Ndipo ophunzirawo anamuka, nachita monga Yesu anawauza;


Nati Iye, Mukani kumzinda kwa munthu wina wake, mukati kwa Iye, Mphunzitsi anena, Nthawi yanga yayandikira; ndidzadya Paska kwanu pamodzi ndi ophunzira anga.


Ndipo pakufika madzulo, Iye analinkukhala pachakudya pamodzi ndi ophunzira khumi ndi awiri;


Muli abwenzi anga inu, ngati muzichita zimene ndikulamulani inu.


Amake ananena kwa atumiki, Chimene chilichonse akanena kwa inu, chitani.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa