Mateyu 25:4 - Buku Lopatulika4 koma anzeruwo anatenga mafuta m'nsupa zao, pamodzi ndi nyali zao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 koma anzeruwo anatenga mafuta m'nsupa zao, pamodzi ndi nyali zao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Koma asanu ochenjera aja adaatenga mafuta ena apadera m'nsupa zao. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 koma ochenjerawo anatenga mafuta awo mʼmabotolo pamodzi ndi nyale zawo. Onani mutuwo |