Mateyu 25:5 - Buku Lopatulika5 Ndipo pamene mkwati anachedwa, onsewo anaodzera, nagona tulo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Ndipo pamene mkwati anachedwa, onsewo anaodzera, nagona tulo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Popeza kuti mkwati adaachedwa, onse aja adayamba kuwodzera, nagona tulo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Mkwati anachedwa ndipo onse anayamba kusinza nagona. Onani mutuwo |