Mateyu 24:8 - Buku Lopatulika8 Koma ndizo zonsezi zowawa zoyamba. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Koma ndizo zonsezi zowawa zoyamba. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Tsono zonsezitu nkuyamba chabe kwa mavuto. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Zonsezi ndi chiyambi chabe cha zowawa. Onani mutuwo |