Mateyu 24:40 - Buku Lopatulika40 Pomwepo adzakhala awiri m'munda; mmodzi adzatengedwa, ndi wina adzasiyidwa: Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201440 Pomwepo adzakhala awiri m'munda; mmodzi adzatengedwa, ndi wina adzasiyidwa: Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa40 Pa nthaŵi imeneyo anthu aŵiri adzakhala ali m'munda, mmodzi adzamtenga, winayo nkumusiya. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero40 Amuna awiri adzakhala mʼmunda; wina adzatengedwa ndi wina adzatsala. Onani mutuwo |