Mateyu 24:41 - Buku Lopatulika41 awiri adzakhala opera pamphero; mmodzi adzatengedwa, ndi wina adzasiyidwa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201441 awiri adzakhala opera pamphero; mmodzi adzatengedwa, ndi wina adzasiyidwa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa41 Azimai aŵiri adzakhala akusinja, mmodzi adzamtenga, winayo nkumusiya. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero41 Amayi awiri adzakhala akusinja pa mtondo; wina adzatengedwa ndi wina adzatsala. Onani mutuwo |