Mateyu 24:4 - Buku Lopatulika4 Ndipo Yesu anayankha nati kwa iwo, Yang'anirani, asasokeretse inu munthu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Ndipo Yesu anayankha nati kwa iwo, Yang'anirani, asasokeretse inu munthu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Yesu adaŵayankha kuti, “Chenjerani kuti wina aliyense asadzakusokezeni. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Yesu anayankha kuti, “Onetsetsani kuti wina asakunyengeni. Onani mutuwo |