Mateyu 24:5 - Buku Lopatulika5 Pakuti ambiri adzafika m'dzina langa, nadzanena, Ine ndine Khristu, nadzasokeretsa anthu ambiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Pakuti ambiri adzafika m'dzina langa, nadzanena, Ine ndine Khristu, nadzasokeretsa anthu ambiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Chifukwa kudzafika anthu ambiri m'dzina langa namadzanena kuti, ‘Mpulumutsi wolonjezedwa uja ndine,’ ndipo adzasokeza anthu ambiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Pakuti ambiri adzabwera mʼdzina langa nadzati, ‘Ndine Khristu,’ ndipo adzanyenga ambiri. Onani mutuwo |