Mateyu 24:36 - Buku Lopatulika36 Koma za tsiku ili ndi nthawi yake saidziwa munthu aliyense, angakhale angelo a Kumwamba, kapena Mwana, koma Atate yekha. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201436 Koma za tsiku ili ndi nthawi yake sadziwa munthu aliyense, angakhale angelo a Kumwamba, kapena Mwana, koma Atate yekha. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa36 “Koma za tsiku lake kapena nthaŵi yake, palibe amene amadziŵa. Angelo omwe akumwamba sadziŵa. Ngakhale Ineyo Mwanane sindidziŵa; amadziŵa ndi Atate okha basi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero36 “Palibe amene adziwa za tsikulo kapena nthawi, angakhale angelo akumwamba, angakhale Mwana, koma Atate okha. Onani mutuwo |