Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Mateyu 24:18 - Buku Lopatulika

18 ndi iye wa m'munda asabwere kutenga chofunda chake.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

18 ndi iye wa m'munda asabwere kutenga chofunda chake.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

18 Yemwe ali ku munda, asabwererenso ku nyumba kuti akatenge mwinjiro.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

18 Yemwe ali ku munda asapite kukatenga mkanjo wake.

Onani mutuwo Koperani




Mateyu 24:18
4 Mawu Ofanana  

Nanena naye mfumu, Ufunanji? Nati iye, Mnzanga uyu ananena ndi ine, Tenga mwana wako timudye lero, ndi mwana wanga timudye mawa.


iye ali pamwamba pa tsindwi, asatsikire kunyamula za m'nyumba mwake;


Koma tsoka ali nalo iwo akukhala ndi pakati, ndi akuyamwitsa ana m'masiku awo!


Tsikulo iye amene adzakhala pamwamba pa tsindwi, ndi akatundu ake m'nyumba, asatsike kuwatenga; ndipo iye amene ali m'munda modzimodzi asabwere ku zake za m'mbuyo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa