Mateyu 24:17 - Buku Lopatulika17 iye ali pamwamba pa tsindwi, asatsikire kunyamula za m'nyumba mwake; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 iye ali pamwamba pa chindwi, asatsikire kunyamula za m'nyumba mwake; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Amene ali padenga pa nyumba yake, asatsike nkuloŵanso m'nyumba mwake kuti akatenge katundu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Yemwe ali pa denga la nyumba yake asatsike kukatulutsa chinthu chilichonse mʼnyumba. Onani mutuwo |