Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Mateyu 24:12 - Buku Lopatulika

12 Ndipo chifukwa cha kuchuluka kwa kusaweruzika, chikondano cha anthu aunyinji chidzazilala.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

12 Ndipo chifukwa cha kuchuluka kwa kusaweruzika, chikondano cha anthu aunyinji chidzazilala.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

12 Tsono popeza kuti zoipa zizidzachulukirachulukira, chikondi chizidzacheperachepera pakati pa anthu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

12 Chifukwa cha kuchuluka kwa zoyipa, chikondi cha ambiri chidzazirala,

Onani mutuwo Koperani




Mateyu 24:12
8 Mawu Ofanana  

Ndipo aneneri onama ambiri adzauka, nadzasokeretsa anthu ambiri.


Koma iye wakulimbika chilimbikire kufikira kuchimaliziro, yemweyo adzapulumuka.


Mwa ichi, mutavula chinyanso chonse ndi chisefukiro cha choipa, landirani ndi chifatso mau ookedwa mwa inu, okhoza kupulumutsa moyo wanu.


Usaope zimene uti udzamve kuwawa; taona, mdierekezi adzaponya ena a inu m'nyumba yandende, kuti mukayesedwe; ndipo mudzakhala nacho chisautso masiku khumi. Khala wokhulupirika kufikira imfa, ndipo ndidzakupatsa iwe korona wa moyo.


Ndidziwa ntchito zako, kuti suli wozizira kapena wotentha: mwenzi utakhala wozizira kapena wotentha.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa