Mateyu 24:11 - Buku Lopatulika11 Ndipo aneneri onama ambiri adzauka, nadzasokeretsa anthu ambiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Ndipo aneneri onama ambiri adzauka, nadzasokeretsa anthu ambiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Kudzaoneka aneneri onama ambiri, amene azidzasokeza anthu ambiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 ndipo aneneri onama ambiri adzaoneka ndi kunyenga anthu ambiri. Onani mutuwo |