Mateyu 24:10 - Buku Lopatulika10 Ndipo pomwepo ambiri adzakhumudwa, nadzaperekana wina ndi mnzake, nadzadana wina ndi mnzake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Ndipo pomwepo ambiri adzakhumudwa, nadzaperekana wina ndi mnzake, nadzadana wina ndi mnzake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Pa nthaŵi imeneyo ambiri adzataya chikhulupiriro chao, azidzaperekana nkumadana. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Pa nthawi imeneyo ambiri adzasiya chikhulupiriro ndipo adzadana ndi kuperekana wina ndi mnzake, Onani mutuwo |