Mateyu 23:9 - Buku Lopatulika9 Ndipo inu musatchule wina atate wanu pansi pano, pakuti alipo mmodzi ndiye Atate wanu wa Kumwamba. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Ndipo inu musatchule wina atate wanu pansi pano, pakuti alipo mmodzi ndiye Atate wanu wa Kumwamba. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Musamatchulanso munthu pansi pano kuti atate, popeza kuti muli ndi atate amodzi okha, ndiwo Atate anu akumwamba. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Ndipo musamatchule wina aliyense pansi pano kuti ‘Atate,’ pakuti muli ndi Atate mmodzi, ndipo ali kumwamba. Onani mutuwo |