Mateyu 23:10 - Buku Lopatulika10 Ndipo musatchedwa atsogoleri, pakuti alipo mmodzi Mtsogoleri wanu, ndiye Khristu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Ndipo musatchedwa atsogoleri, pakuti alipo mmodzi Mtsogoleri wanu, ndiye Khristu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Anthu asatinso azikutchulani atsogoleri, popeza kuti Mtsogoleri wanu ndi mmodzi yekha, ndiye Khristu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Komanso musamatchedwenso ‘Mtsogoleri,’ pakuti muli naye Mtsogoleri mmodzi amene ndi Khristu. Onani mutuwo |