Mateyu 23:21 - Buku Lopatulika21 Ndipo wakulumbira kutchula Kachisi, alumbira ameneyo ndi Iye wakukhala momwemo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Ndipo wakulumbira kutchula Kachisi, alumbira ameneyo ndi Iye wakukhala momwemo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Akalumbira kuti, Pali Nyumba ya Mulungu, walumbiranso pa zonse zimene zili m'Nyumbamo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Ndipo iye wolumbira potchula Nyumba ya Mulungu alumbira pa Nyumbayo ndi pa Iye amene amakhala mʼmenemo. Onani mutuwo |