Mateyu 23:22 - Buku Lopatulika22 Ndipo wakulumbira kutchula Kumwamba, alumbira chimpando cha Mulungu, ndi Iye wakukhala pomwepo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 Ndipo wakulumbira kutchula Kumwamba, alumbira chimpando cha Mulungu, ndi Iye wakukhala pomwepo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 Ndipo akalumbira kuti, Kumwambadi, walumbiranso pa mpando wachifumu wa Mulungu, ndiponso pa Iye amene amakhala pampandopo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 Ndipo iye wolumbira kutchula kumwamba alumbira kutchula mpando waufumu wa Mulungu ndi pa Iye wokhalapo. Onani mutuwo |