Mateyu 23:20 - Buku Lopatulika20 Chifukwa chake wakulumbira kutchula guwa la nsembe, alumbira limenelo ndi zonse za pamwamba pake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 Chifukwa chake wakulumbira kutchula guwa la nsembe, alumbira limenelo ndi zonse za pamwamba pake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 Tsonotu munthu akalumbira kuti, Pali guwa la nsembe, walumbiranso pa zonse zimene zili paguwapo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 Chifukwa chake, iye amene alumbira kutchula guwa alumbira pa ilo ndi pa chilichonse chili pamenepo. Onani mutuwo |