Mateyu 22:34 - Buku Lopatulika34 Koma Afarisi, pakumva kuti Iye anatontholetsa Asaduki, anasonkhana. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201434 Koma Afarisi, pakumva kuti Iye anatontholetsa Asaduki, anasonkhana. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa34 Afarisi atamva kuti Yesu adatsutsa Asaduki, adasonkhana. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero34 Pakumva kuti Yesu anawakhalitsa chete Asaduki, Afarisi anasonkhana pamodzi. Onani mutuwo |