Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Mateyu 22:33 - Buku Lopatulika

33 Ndipo pamene makamu a anthu anamva, anazizwa ndi chiphunzitso chake.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

33 Ndipo pamene makamu a anthu anamva, anazizwa ndi chiphunzitso chake.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

33 Pamene anthu ochuluka aja amene anali pamenepo adamva zimenezi, adadabwa kwambiri ndi zophunzitsa zake.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

33 Magulu a anthu atamva zimenezi, anazizwa ndi chiphunzitso chake.

Onani mutuwo Koperani




Mateyu 22:33
8 Mawu Ofanana  

Ndipo pamene iwo anamva, anazizwa, namsiya Iye, nachokapo.


Ndipo Yesu anati kwa iwo, Perekani zake za Kaisara kwa Kaisara, ndi zake za Mulungu kwa Mulungu. Ndipo anazizwa naye kwambiri.


Ndipo pofika tsiku la Sabata, anayamba kuphunzitsa m'sunagoge; ndipo ambiri anamva Iye, nazizwa, nanena, Uyu adazitenga kuti izi? Nzeru yopatsidwa kwa munthuyu njotani, ndi zamphamvu zotere zochitidwa ndi manja ake?


Ndipo onse amene anamva Iye anadabwa ndi chidziwitso chake, ndi mayankho ake.


Ndipo onse anamchitira Iye umboni nazizwa ndi mau a chisomo akutuluka m'kamwa mwake; nanena, Kodi uyu si mwana wa Yosefe?


Anyamatawo anayankha, Nthawi yonse palibe munthu analankhula chotero.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa