Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Mateyu 22:35 - Buku Lopatulika

35 Ndipo mmodzi wa iwo, mphunzitsi wa malamulo, anamfunsa ndi kumuyesa Iye, nati,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

35 Ndipo mmodzi wa iwo, mphunzitsi wa chilamulo, anamfunsa ndi kumuyesa Iye, nati,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

35 Tsono mmodzi mwa iwo, katswiri wa Malamulo, adafunsa Yesu funso kuti amutape m'kamwa.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

35 Mmodzi wa iwo, katswiri wa malamulo anamuyesa Iye ndi funso ndipo anati,

Onani mutuwo Koperani




Mateyu 22:35
10 Mawu Ofanana  

Koma Yesu anadziwa kuipa kwao, nati, Mundiyeseranji Ine, onyenga inu?


Mphunzitsi, lamulo lalikulu ndi liti la m'chilamulo?


Ndipo anadza kwa Iye Afarisi, namfunsa Iye ngati kuloledwa kuti munthu achotse mkazi wake, namuyesa Iye.


Tsoka inu, achilamulo! Chifukwa munachotsa chifungulo cha nzeru; inu simunalowamo nokha, ndipo munawaletsa iwo analinkulowa.


Ndipo Yesu anayankha nati kwa achilamulo ndi Afarisi, nanena, Kodi nkuloledwa tsiku la Sabata kuchiritsa, kapena iai?


Koma Afarisi ndi achilamulo anakaniza uphungu wa Mulungu kwa iwo okha, popeza sanabatizidwe ndi iye.


Koma ichi ananena kuti amuyese Iye, kuti akhale nacho chomneneza Iye. Koma Yesu, m'mene adawerama pansi analemba pansi ndi chala chake.


Zena nkhoswe ya milandu, ndi Apolo ufulumire kuwakonzera zaulendo, kuti asasowe kanthu,


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa