Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Mateyu 22:31 - Buku Lopatulika

31 Koma za kuuka kwa akufa, simunawerenge kodi chomwe chinanenedwa kwa inu ndi Mulungu, kuti,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

31 Koma za kuuka kwa akufa, simunawerenga kodi chomwe chinanenedwa kwa inu ndi Mulungu, kuti,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

31 Tsono zakuti anthu adzauka kwa akufa, kodi simudaŵerenge zimene Mulungu adakuuzani zija kuti,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

31 Koma za kuukitsidwa kwa akufa, kodi simunawerenge zimene Mulungu ananena kwa inu kuti,

Onani mutuwo Koperani




Mateyu 22:31
7 Mawu Ofanana  

Koma Iye anati kwa iwo, Kodi simunawerenge chimene anachichita Davide, pamene anali ndi njala, ndi iwo amene anali naye?


Koma mukadadziwa nchiyani ichi, Ndifuna chifundo, si nsembe ai; simukadaweruza olakwa iwo osachimwa,


nanena kwa Iye, Mulinkumva kodi chimene alikunena awa? Ndipo Yesu ananena kwa iwo, Inde: simunawerenge kodi, M'kamwa mwa makanda ndi oyamwa munafotokozera zolemekeza?


Yesu ananena kwa iwo, Kodi simunawerenge konse m'malembo, Mwala umene anaukana omanga nyumba womwewu unakhala mutu wa pangodya: Ichi chinachokera kwa Ambuye, ndipo chili chozizwitsa m'maso mwathu?


Pakuti m'kuuka kwa akufa sakwatira, kapena kukwatiwa, koma akhala ngati angelo a Kumwamba.


Ine ndili Mulungu wa Abrahamu, ndi Mulungu wa Isaki, ndi Mulungu wa Yakobo? Sali Mulungu wa akufa koma wa amoyo.


Koma mukani muphunzire nchiyani ichi, Ndifuna chifundo, si nsembe ai; pakuti sindinadze kudzaitana olungama, koma ochimwa.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa