Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Mateyu 22:25 - Buku Lopatulika

25 Tsono panali ndi ife abale asanu ndi awiri; ndipo wakuyamba anakwatira, namwalira wopanda mbeu, nasiyira mphwake mkazi wake;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

25 Tsono panali ndi ife abale asanu ndi awiri; ndipo wakuyamba anakwatira, namwalira wopanda mbeu, nasiyira mphwake mkazi wake;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

25 Tsono kwathu kudaali anthu asanu ndi aŵiri pachibale pao. Woyamba adaakwatira mkazi, nkumwalira. Tsono popeza kuti analibe mwana, adasiyira mbale wake mkazi wake uja.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

25 Tsopano panali abale asanu ndi awiri pakati pathu. Woyambayo anakwatira ndipo anamwalira, ndipo popeza analibe ana, mʼbale wake analowa chokolo.

Onani mutuwo Koperani




Mateyu 22:25
5 Mawu Ofanana  

nanena, Mphunzitsi, Mose anati, Ngati munthu akafa wopanda mwana, mphwake adzakwatira mkazi wake, nadzamuukitsira mbale wake mbeu.


chimodzimodzi wachiwiri, ndi wachitatu, kufikira wachisanu ndi chiwiri.


Ndipo popeza kwaikikatu kwa anthu kufa kamodzi, ndipo atafa, chiweruziro;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa