Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Mateyu 22:26 - Buku Lopatulika

26 chimodzimodzi wachiwiri, ndi wachitatu, kufikira wachisanu ndi chiwiri.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

26 chimodzimodzi wachiwiri, ndi wachitatu, kufikira wachisanu ndi chiwiri.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

26 Chimodzimodzinso wachiŵiri ndi wachitatu, mpaka wachisanu ndi chiŵiri.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

26 Izi zinachitikiranso mʼbale wa chiwiri ndi wachitatu mpaka wachisanu ndi chiwiri.

Onani mutuwo Koperani




Mateyu 22:26
4 Mawu Ofanana  

Asumwa, sayankhanso, Anawathera mau.


Ndipo anatumiza kwa Iye ophunzira ao, pamodzi ndi Aherode, amene ananena, Mphunzitsi, tidziwa kuti muli woona, ndipo muphunzitsa njira ya Mulungu moona ndithu, ndipo simusamala munthu aliyense; pakuti simuyang'anira pa nkhope ya anthu.


Tsono panali ndi ife abale asanu ndi awiri; ndipo wakuyamba anakwatira, namwalira wopanda mbeu, nasiyira mphwake mkazi wake;


Ndipo pomalizira anamwaliranso mkaziyo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa