Mateyu 22:19 - Buku Lopatulika19 Tandionetsani Ine ndalama yamsonkho. Ndipo iwo anadza nalo kwa Iye rupiya latheka. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Tandionetsani Ine ndalama yamsonkho. Ndipo iwo anadza nalo kwa Iye rupiya latheka. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Tandiwonetsani ndalama yamsonkho.” Iwo adampatsadi ndalamayo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Onetseni ndalama imene mumapereka msonkho.” Iwo anabweretsa dinari, Onani mutuwo |