Mateyu 22:20 - Buku Lopatulika20 Ndipo Iye anati kwa iwo, Ncha yani chithunzithunzi ichi, ndi kulemba kwake? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 Ndipo Iye anati kwa iwo, Ncha yani chithunzithunzi ichi, ndi kulemba kwake? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 Pamenepo Iye adaŵafunsa kuti, “Kodi nkhopeyi ndi ya yani, ndipo dzinali ndi la yani?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 ndipo anawafunsa kuti, “Kodi chithunzi ichi ndi malemba awa ndi za ndani?” Onani mutuwo |