Mateyu 21:23 - Buku Lopatulika23 Ndipo m'mene Iye analowa mu Kachisi, ansembe aakulu ndi akulu a anthu anadza kwa Iye analikuphunzitsa, nanena, Muchita izi ndi ulamuliro wotani? Ndipo ndani anakupatsani ulamuliro wotere? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 Ndipo m'mene Iye analowa m'Kachisi, ansembe aakulu ndi akulu a anthu anadza kwa Iye analikuphunzitsa, nanena, Muchita izi ndi ulamuliro wotani? Ndipo ndani anakupatsani ulamuliro wotere? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 Yesu adaloŵa m'Nyumba ya Mulungu, ndipo pamene ankaphunzitsa, akulu a ansembe ndi akulu a Ayuda adadzamufunsa kuti, “Kodi mphamvu zoti muzichita zimenezi mudazitenga kuti? Ndani adakupatsani mphamvu zimenezi?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 Yesu analowa mʼNyumba ya Mulungu, ndipo pamene ankaphunzitsa, akulu a ansembe ndi akuluakulu anabwera kwa Iye namufunsa kuti, “Muchita izi ndi ulamuliro wanji ndipo anakupatsani ndani ulamuliro umenewu?” Onani mutuwo |