Mateyu 21:22 - Buku Lopatulika22 Ndipo zinthu zilizonse mukazifunsa m'kupemphera ndi kukhulupirira, mudzazilandira. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 Ndipo zinthu zilizonse mukazifunsa m'kupemphera ndi kukhulupirira, mudzazilandira. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 Ngati mukhala ndi chikhulupiriro, zonse zimene mungapemphe kwa Mulungu mudzalandira.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 Ngati mukhulupirira, mudzalandira chilichonse chimene muchipempha mʼpemphero.” Onani mutuwo |