Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Mateyu 21:20 - Buku Lopatulika

20 Ndipo ophunzira poona ichi anazizwa, nati, Mkuyuwo unafota bwanji msanga?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

20 Ndipo ophunzira poona ichi anazizwa, nati, Mkuyuwo unafota bwanji msanga?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

20 Pamene ophunzira aja adaona zimenezi, adadabwa nafunsa Yesu kuti, “Mkuyuwu wauma bwanji nthaŵi yomweyi?”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

20 Ophunzira ataona zimenezi, anadabwa nafunsa kuti, “Kodi mtengo wamkuyuwu wauma msanga bwanji?”

Onani mutuwo Koperani




Mateyu 21:20
6 Mawu Ofanana  

Ndipo pakuona mkuyu umodzi panjira, anafika pamenepo, napeza palibe kanthu koma masamba okhaokha; nati Iye kwa uwo, Sudzabalanso chipatso kunthawi zonse. Ndipo pomwepo mkuyuwo unafota.


Ndipo Yesu anayankha, nati kwa iwo, Indedi ndinena kwa inu, Ngati mukhala nacho chikhulupiriro, osakayikakayika, mudzachita si ichi cha pa mkuyu chokha, koma ngati mudzati ngakhale kuphiri ili, Tanyamulidwa, nuponyedwe m'nyanja, chidzachitidwa.


Ndipo pakumva ichi, Yesu anazizwa, nati kwa iwo akumtsata, Indetu ndinena kwa inu, ngakhale mwa Israele, sindinapeze chikhulupiriro chotere.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa