Mateyu 21:18 - Buku Lopatulika18 Ndipo mamawa, m'mene Iye analinkunkanso kumzinda, anamva njala. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Ndipo mamawa, m'mene Iye analinkunkanso kumzinda, anamva njala. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 M'maŵa mwake, m'mamaŵa ndithu, pamene Yesu ankabwerera ku Yerusalemu, adaamva njala. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Mmamawa, pamene amabwera ku mzinda, anamva njala. Onani mutuwo |