Mateyu 20:4 - Buku Lopatulika4 ndipo kwa iwo anati, Pitani inunso kumunda, ndipo ndidzakupatsani chimene chili choyenera. Ndipo iwo anapita. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 ndipo kwa iwo anati, Pitani inunso kumunda, ndipo ndidzakupatsani chimene chili choyenera. Ndipo iwo anapita. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Adaŵauza kuti, ‘Inunso pitani ku munda wanga wamphesa, ndidzakulipirani moyenerera.’ Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Anawawuza kuti, ‘Inunso pitani mukagwire ntchito mʼmunda wanga wa mpesa, ndipo ndidzakulipirani malipiro oyenera.’ Onani mutuwo |