Mateyu 20:5 - Buku Lopatulika5 Ndiponso anatuluka usana, ndimonso popendeka dzuwa, nachita chimodzimodzi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Ndiponso anatuluka usana, ndimonso popendeka dzuwa, nachita chimodzimodzi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Iwowo adapitadi. Munthu uja adapitanso pa 12 koloko masana ndi pa 3 koloko, nakachita chimodzimodzi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Ndipo anapita. “Anatulukanso nthawi ya 12 koloko masana, ndi nthawi ya 3 koloko masananso nachita chimodzimodzi. Onani mutuwo |