Mateyu 20:3 - Buku Lopatulika3 Ndipo anatuluka dzuwa litakwera, naona ena ataima chabe pabwalo; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Ndipo anatuluka dzuwa litakwera, naona ena ataima chabe pabwalo; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Pa nthaŵi ya 9 koloko adapitanso, nakapeza ena atangokhala khale pa msika, osagwira ntchito. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 “Nthawi 9 koloko mmawa, anatulukanso naona ena atayimirira pa msika akungokhala. Onani mutuwo |