Mateyu 20:29 - Buku Lopatulika29 Ndipo pamene iwo analikutuluka mu Yeriko, khamu lalikulu la anthu linamtsata Iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201429 Ndipo pamene iwo analikutuluka m'Yeriko, khamu lalikulu la anthu linamtsata Iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa29 Pamene Yesu ndi ophunzira ake ankatuluka mu mzinda wa Yeriko, anthu ambirimbiri ankamutsatira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero29 Pamene Yesu ndi ophunzira ake ankachoka ku Yeriko, gulu lalikulu la anthu linawatsata. Onani mutuwo |