Mateyu 20:16 - Buku Lopatulika16 Chomwecho omalizira adzakhala oyamba, ndipo oyamba adzakhala omalizira. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Chomwecho omalizira adzakhala oyamba, ndipo oyamba adzakhala omalizira. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Tsono Yesu adati, “Choncho amene ali oyambirira adzakhala otsirizira. Ndipo amene ali otsirizira adzakhala oyambirira.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 “Momwemo omalizira adzakhala oyamba ndipo oyamba adzakhala omalizira.” Onani mutuwo |