Mateyu 20:17 - Buku Lopatulika17 Ndipo pamene Yesu analikukwera ku Yerusalemu, anatenga ophunzira khumi ndi awiri napita nao pa okha, ndipo panjira anati kwa iwo, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Ndipo pamene Yesu analikukwera ku Yerusalemu, anatenga ophunzira khumi ndi awiri napita nao pa okha, ndipo panjira anati kwa iwo, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Pamene Yesu ankapita ku Yerusalemu, adaŵatengera pambali ophunzira ake khumi ndi aŵiri aja. Pa njira adaŵauza kuti, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Tsopano pamene Yesu ankapita ku Yerusalemu, anatengera pambali ophunzira ake khumi ndi awiriwo nati kwa iwo, Onani mutuwo |