Mateyu 20:14 - Buku Lopatulika14 Tenga lako, numuke; pakuti ine ndifuna kupatsa kwa uyu womalizira monga kwa iwe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Tenga lako, numuke; pakuti ine ndifuna kupatsa kwa uyu womalizira monga kwa iwe. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Tenga malipiro ako, uzipita. Mwiniwakene ndafuna kuti ndipatse wolembedwa potsirizayu molingana ndi iwe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Tenga malipiro ako pita. Ndikufuna kumupatsa munthu amene ndinamulemba pomaliza mofanana ndi mmene ndakupatsira iwe. Onani mutuwo |