Mateyu 2:20 - Buku Lopatulika20 nati, Tauka, nutenge kamwana ndi amake, nupite kudziko la Israele: chifukwa anafa uja wofuna moyo wake wa kamwanako. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 nati, Tauka, nutenge kamwana ndi amake, nupite kudziko la Israele: chifukwa anafa uja wofuna moyo wake wa kamwanako. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 Adamuuza kuti, “Nyamuka, tenga mwanayu ndi mai wake, ubwerere ku Israele. Aja ankafuna kumupha mwanayu adafa.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 nanena kuti, “Nyamuka, tenga mwanayo ndi amayi ake ndipo mupite ku dziko la Israeli, popeza amene anafuna moyo wa mwanayo anamwalira.” Onani mutuwo |