Mateyu 2:21 - Buku Lopatulika21 Ndipo anauka iye, natenga kamwana ndi amake, nalowa m'dziko la Israele. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Ndipo anauka iye, natenga kamwana ndi amake, nalowa m'dziko la Israele. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Apo Yosefe adanyamuka, nkutenga mwana uja ndi mai wake, kubwerera ku Israele. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Tsono Yosefe atadzuka anatenga mwanayo ndi amayi ake kupita ku dziko la Israeli. Onani mutuwo |