Mateyu 2:19 - Buku Lopatulika19 Koma pakumwalira Herode, onani, mngelo wa Ambuye anaonekera m'kulota kwa Yosefe mu Ejipito, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Koma pakumwalira Herode, onani, mngelo wa Ambuye anaonekera m'kulota kwa Yosefe m'Ejipito, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Herode atamwalira, mngelo wa Ambuye adaonekera Yosefe m'maloto ku Ejipito. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Atamwalira Herode, mngelo wa Ambuye anaonekera kwa Yosefe mʼmaloto ku Igupto Onani mutuwo |