Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Mateyu 2:14 - Buku Lopatulika

14 Ndipo iye ananyamuka natenga kamwana ndi amake usiku, nachoka kupita ku Ejipito;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

14 Ndipo iye ananyamuka natenga kamwana ndi amake usiku, nachoka kupita ku Ejipito;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

14 Apo Yosefe adadzuka usiku womwewo, nkutenga mwanayo ndi mai wake kupita ku Ejipito.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

14 Atadzuka, Yosefe anatenga mwanayo ndi amayi ake usiku omwewo napita ku Igupto,

Onani mutuwo Koperani




Mateyu 2:14
6 Mawu Ofanana  

Ndipo Yosefe anauka tulo take, nachita monga anamuuza mngelo wa Ambuye, nadzitengera yekha mkazi wake;


Ndipo pamene iwo anachoka, onani, mngelo wa Ambuye anaonekera kwa Yosefe m'kulota, nati, Tauka, nutenge kamwanako ndi amake, nuthawire ku Ejipito, nukakhale kumeneko kufikira ndidzakuuza iwe; pakuti Herode adzafuna kamwana kukaononga Iko.


nakhalabe kumeneko kufikira atamwalira Herode; kuti chikachitidwe chonenedwa ndi Ambuye mwa mneneri kuti, Ndinaitana Mwana wanga atuluke mu Ejipito.


Ndipo anadza kwa Iye, namuutsa, nanena, Ambuye, Ambuye, titayika. Ndipo anauka, nadzudzula mphepo ndi mafunde ake a madzi; pomwepo zinaleka, ndipo panagwa bata.


Chifukwa cha izi Ayuda anandigwira mu Kachisi, nayesa kundipha.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa