Mateyu 19:6 - Buku Lopatulika6 Chotero kuti salinso awiri koma thupi limodzi. Chifukwa chake ichi chimene Mulungu anachimanga pamodzi, munthu asachilekanitse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Chotero kuti salinso awiri koma thupi limodzi. Chifukwa chake ichi chimene Mulungu anachimanga pamodzi, munthu asachilekanitse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Choncho tsopano salinso aŵiri koma thupi limodzi. Tsono zimene Mulungu wazilumukiza pamodzi, munthu asazilekanitse.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Motero salinso awiri ayi koma mmodzi. Nʼchifukwa chake chimene Mulungu wachimanga pamodzi munthu wina asachilekanitse.” Onani mutuwo |